Kufotokozera
kulondoloza ndi pulogalamu yomwe imapereka liwu kwa a Malawi kuti azionesetsa kuti adindo akufotokozera ntchitio zomwe akugwira kwa nzika za dziko
Kulondoloza ndi kukambirana kwa pakati pa boma ndi nzika za dziko lino pa nkhani zokhudza kasamalidwe ka chuma cha dziko pofuna kupititsa patsogolo chitukuko cha dziko lathu, la Malawi.